lirik lagu uncle short one – langwan piksy
chi piksy chinfarner chodziwiker ndi boumurr
chorus
hey uncle
uncle short-one
mukuganizira zotani
uncle short-one
kuno ngini yakuphonyani
uncle short-one
ndikale lija munatchona inu
uncle short-one
kuno mb-mba yakusowani
verse one
maloto awa tinayambira limodzi
sitinaganizire zinthu zingafike chonchi
mmaso mwa ine ya chimwemwe misonzi
oh i wish mukanakhala kuno nkozi
my uncle komanso my best friend
munkandiuza chirichonse munali open
nd-nkadzanena kwa inu ndikayiputa ndeu
kamunthu kakafupi koma simakani akewo
pena ndimaseka……ndekha
munkati mukakwiya munkadzitchula undertaker
nkhani za inu zambiri zongopeka
pano ndinakula munkathoka ngini yosatheka
(laugh)
i called you biggie
munali nane olo weather ingakhale windy
muzambiri munandipanga lead
i’m a man now pano ndidziwa zambiri
chorus
verse two
munkanena kuti zinthu zidzayenda
one day….dollar ndidza spenda
munkanena ndidzaphula if i work hard
one day… zakale ndidzagenda
ndikakhala duuu
kuk-mbuka kale lathu
tinkasowa zinthu
munaganizano zongotuuu… luka
koma zonse munanena sindin-z-taye
ngakhale ngini inashupa sindinagwe mphwayi
mulungu anandidalitsa inakwana nthawi
kunyada kwa abambo anga chimwemwe cha mayi
ngini bho panopa i’m doing awesome
pano ndinapeza aine ma bouncer
pamene pankawopsapo pano ndinadutsa
mulungu anachotsa zonse zinkasautsa
chorus
verse three
ndikasekelera ndinuyo ndimak-mbukira
ndikanakondwera mukanakhala mwafupikira
kwa inu… zambiri ndinaphunzira
munkandiuza madalitso adzandikhuthukira
mukanakhalapo mukanamva kukoma
nephew wanu akudziwika ndi boma
anakula pano anapeza kadona
uncle…nephew wanu anablowa
success yanga inabwera ngati heart attack
ndikanena zinthu amayesa ndikulalata
luso lija lik-mabweretsa dollar
zimene zinkapinga zija ambuye anathyola
mulungu anatsegula kh-m-
nephew wanu panopa ndi role model
ndakusowani
uncle short-one
ndine wanu wanu langwan
chorus
outro
ndefeyo entertainment
lirik lagu lainnya :
- kumpulan lirik lagu amy ly › lirik lagu this isn’t where it ends – amy ly
- kumpulan lirik lagu theinvaezn › lirik lagu lose my mind – theinvaezn
- kumpulan lirik lagu de saiyajin › lirik lagu look, love, poxa crush – dé saiyajin
- kumpulan lirik lagu phil fresh › lirik lagu it’s me – phil fresh
- kumpulan lirik lagu lusive › lirik lagu vibe on me – lusive
- kumpulan lirik lagu lofficina della camomilla › lirik lagu gommaragno – demo – l’officina della camomilla
- kumpulan lirik lagu dony cole › lirik lagu jayfake diss – dony cole
- kumpulan lirik lagu yoshua › lirik lagu matthew in the middle – yoshua
- kumpulan lirik lagu jacexy › lirik lagu molly savage (remix) – jacexy
- kumpulan lirik lagu jizza raw › lirik lagu take you – jizza raw