lirikcinta.com
a b c d e f g h i j k l m n o p q r s t u v w x y z 0 1 2 3 4 5 6 7 8 9 #

lirik lagu kwathu sipadziko – innocent p. makuwira

Loading...

kwathu sipadziko ndingopitilira;
ndazikundikira chuma k-mwambako
mngelo akodola pakh-m- lammwamba
ndipo dziko lapansi sindiyesa kwathu.
mbuye ndinu bwenzi langa ndithu
ndichitenji ngati k-mwambako sikwathu
mngelo akodola pakh-m- lammwamba
ndipo dziko lapansi sindiyesa kwathu.
mayi watsogola muulemelero
ndifuna kugwira dzanja lake, konko
andiyembekeza chinthuchi ndidziwa
ndipo dziko lapansi sindiyesa kwathu

lirik lagu lainnya :

YANG LAGI NGE-TRENDS...

Loading...