lirikcinta.com
a b c d e f g h i j k l m n o p q r s t u v w x y z 0 1 2 3 4 5 6 7 8 9 #

tiziti mwayiwala? - mfumu hyphen lyrics

Loading...

[intro: che kalonda]
don’t get too comfortable iyayi
basi k*makhala, k*mazinamiza ayi ine ndi wakuti wakuti
ine ndi ndani ndani, eeh aise iwe
dziko limasankhatu kuti awawa akhale mbali ya uku
awa akhale mbali ya uku
dziko limasankha si chirichonse mukuyenera kupanga nawo
penapake kungovomereza kuti alipo ena ake
anthu osankhidwa

kukankha mukukankha, koma simumatha
tiziti mwayiwala? ufumu ndi w*nga
tiziti mwayiwala? [?]
tiziti mwayiwala? ufumu ndi w*nga

[verse 1]
eeyoh!
my reign is forever, forever ever
makape ndawaona litsiro
ngini yake itiyo mukusimbwirayo
nyimbo zonse nthabwala ngati winiko
kamandinyasa ine ndi kachisimo
kofuna kufufuta mbiri ko
munthu n’nali pompa when they popped out
i am the one that cut the umbilical
koma now i don’t feel the connection
and these are my offspring, it’s spiritual
like channeling biggiе & pac
you’d swear these vеrses are off of a ouija board
game inasolobana rappers are anything kupatula lyrical
busy kutibwatika ngini zopanda flavor, zopanda nsinjiro
komabe sititopa kukankha (ah ah), mentality ya mamba
delivery ya azamba, calmness ya kachamba
when you’re this real and you’ve been him
magaye sasowa chokamba
koma 3 minutes and change on a track
popanda chimene tamva
[hook: princess multikey & mfumu hyphen]
magaye muzitolele
hold my crown, i’m holding it down
i’m the ring master, enawa ma clown
we set the pace, they follow the sound
tagwira, tagwira, tagwira kaye
tagwira, tagwira, tagwira kaye
tagwira, tagwira, tagwira kaye
zoti ndiine shatta, usayiwale

[verse 2]
kuti tifike pogawana nkate
it’s got to be worth while
mafana akhate kufuna kutchuka
touching my textile
akukudandaulani ma fan, ma bundle kubetsa
mumathadi ku flexa
koma zanyimbo zokhazo tikhoza kuletsa
mwati, wanyamula mbendera nda?
akungoyimba nyimbo zobela nda?
madolo ak*mvera nda?
akuchita k*mveka kugwera nda?
mwachuluka kuvekana ma title, atambwali k*metana
ena mpakana anasiya kutifila chif*kwa tinakana ku worka nawo
i understand the agenda, magaye amawona ngati zophweka
pano akulakalaka titasiya, mwina nawo ndik*mveka
but, osandiyankhula, maka maka ndikautunga
mphw*nga tasuntha, osamakuwa
bp yanga sichedwa ku shooter iwe
[outro]
tiziti mwayiwala? ufumu ndi w*nga
tiziti mwayiwala? [?]
[?]

Random Song Lyrics :

Popular

Loading...