lirik lagu ngati mzimbe – trap squad
intro [revolver]
trap squad aise
royal fam
yeah
verse 1 [revolver]
zimakoma k-mathelo ngati bus ya kwa jali
nkhawa utapanga burry ngati braz ya patali
chapatali timakhala ngati tapenga
mkazi w-nga wa mmaloto uja ndampeza
akandinong’oneza zam’dziko ndimapanga mute
amvekele my crooked smile is kinda cute
unali kuti moyo w-nga wonseu
you make a g turn soft when you say you-gotta go
ati kwada is the reason
ndinamuwuza usapite ngati chisoni
baby you’re the cure to my disease
mtima w-nga umandipweteka when you leave
gave you my heart do with it as you please
i wish i could take this moment and freeze
usakaike ndiwe w-nga basi
ndikamatchila ndi iwe zimakhala ngati
mzimbe
chorus [sir patricks, stich fray]
ngati mzimbe ukomela ku msinde
ngati tulo likoma ku mbanda kucha
tikamacheza usapite honey usapite
tikamacheza ngati usapite honey usapite tizicheza
verse 2 [chavura]
sweet ndingofila bho man
ndavaya kwao wandishophela ka yogurt
which ndingomwela stroll man
wa awuza ana panja kuti chokani
muti sokoneza
muti phokosela ndamugwila nkhosi easy k-munong’oneza
wandipasa kiss ngati barabas
mkazi uyu ine ndimupasa mwana basi
mkulu wina anamdyesa nazo nyani
atakomedwa kutchatisa ka mkazi
anachita kufasa kukombezela msuzi
osadziwa kuti akudya barboon
me anandiuza i love you
ndakuphikila zokoma iwe top goon
nnamupasa kaye mphaka alawe portion
sukudziwa mwina mfana wathila poison
(back to chorus)
verse 3
[sir patricks]
umalasa mtima ukatulukila
ukati honey ndabwela kuzakuphikila
pachisoni kachikondi amazembelera
poti ndimadziwa wabwela za temporaly posachedwa usanzika
[stich fray]
mutu w-nga umazungulira
zimandivuta mtimawu kuwugwila ine
ndikakuona iwe ukupita
mu mtima mumawawa mutu umawawa
kuganizila zina
sizitheka ndipo sindimaona mdima
tingokwatila mwina
its hard to watch you go ndipo zili ngati mzimbe
lirik lagu lainnya :
- kumpulan lirik lagu george jones › lirik lagu where grass won’t grow (bradley sessions) – george jones
- kumpulan lirik lagu craca e dani nega › lirik lagu saravá xangô – craca e dani nega
- kumpulan lirik lagu marisela › lirik lagu mi amor por ti – marisela
- kumpulan lirik lagu rita ora › lirik lagu r.i.p (remix) – rita ora
- kumpulan lirik lagu kery james › lirik lagu ce a d’avilissant – kery james
- kumpulan lirik lagu zona ganjah › lirik lagu por mi mismo – zona ganjah
- kumpulan lirik lagu jrftw › lirik lagu suicidal thoughts – jrftw
- kumpulan lirik lagu hichkas › lirik lagu tiripe ma 2 – hichkas
- kumpulan lirik lagu lil st louis › lirik lagu no time – lil st. louis
- kumpulan lirik lagu rozenb › lirik lagu the real deal – rozenb