
impfa nimulandi - alick macheso lyrics
[intro: jonas kasamba]
yeeeeeeh! chesology!
[chorus: al!ck macheso]
impfa nimulandi, nimulandi
inandilanda, kundilanda makolo anga
impfa nimulandi, nimulandi
inandilanda, kundilanda makolo anga amayo
[verse 1: al!ck macheso]
impfa ndikawalala, inandibera
nzanga w*nga, *n*li wachikondi
impfa ndikawalala, inandibera
nzanga w*nga, *n*li wachikondi mayo
[verse 2: al!ck macheso]
anzathu impfa nimulandi, ndithu inatilanda
kutilanda achibwenzi wathu
anzathu impfa nimulandi, ndithu inatilanda
kutilanda anzanga, achibale amayo
[verse 3: al!ck macheso]
impfa siyisankha, khuti uyu ndiwandani imangotenga chabe
impfa siyisankha, khuti uyu ndiwandani imangotenga chabe amayo
[verse 4: al!ck macheso & elton muropa]
liwa ndomoyipi, ekuelingaa, eyi*elinga, golongani nanga
liwabi khumba*khumba, eyi*elinga, eyi*elinga, golongani nanga
(al!ck)
[verse 5: al!ck macheso]
impfa nimulandi anzanga, inandilanda, inandilanda
kundilanga mwana w*nga, omwe ndinabala kundisiya nandilira amayo
anzanga impfa nimulandi, inandilanda, inandilanda
kundlianga munzanga w*nga, *n*li wachikondi
kundisiya chocho
impfa nimulandi amayo, nimulandi ndikawalala
kutilanda makolo athu, omwe anatibala, kutisiya natilira atatee
chabwino makolo athu, mupume muntendere, (k*mwamba muliko mkomwe mukonze malo athu iiyii*yii*yii oooh*aaah!)
chabwino amayi anga mupume muntendere, (k*mwamba muliko amayo mukonze malo anga iiyii*yii*yii oooh*aaah!)
[verse 6]
[?]
Random Song Lyrics :
- great mistakes - the wisconaut lyrics
- face of my city - arvi lyrics
- amor fati - thanasis papakonstantinou lyrics
- trick me - aviators lyrics
- de crăciun - highman (cristian) lyrics
- ti si mi sve - shorty lyrics
- fade - joshua micah lyrics
- violet - even briar lyrics
- cannot kill myself - mannywellz lyrics
- wingless angel - oni boy lyrics