
mundikumbuke - alick macheso lyrics
[verse 1]
mundik*mbuke amayo ndatsala ndeka
mundik*mbuke amayo ndatsala ndeka ine mundik*mbuke
amayo ndatsala ndeka
mundik*mbuke amayo ndatsala ndeka
mundik*mbuke amayo ndatsala ndeka ine mundik*mbuke
amayo ndatsala ndeka
mundik*mbuke amayo ndatsala ndeka
mundik*mbuke amayo ndatsala ndeka ine mundik*mbuke
amayo ndatsala ndeka
mundik*mbuke amayo ndatsala ndeka
mundik*mbuke amayo ndatsala ndeka ine mundik*mbuke
amayo ndatsala ndeka
[verse 2]
amai asanafe anasiya mawu oooohh
amai asanafe anasiya mawu oooohh
udzafune fune moenda bambo ulinawo
udzafune fune moenda bambo ulinawo
udzafune fune moenda bambo ulinawo
udzafune fune moenda bambo ulinawo
[verse 3]
ndili mwana wapancili ine, wokula naamai
ndili mwana wapancili ine, wokula naamai
ndili wamasiye
wokulila muumpawi
ndili wamasiye, wokulila muumpawi
ndili wamasiye ine, wokulila muumpawi
ndili wamasiye ine, wokulila muumpawi
[verse 4]
azimai ancili ana
amasiye mvelani
azimai ancili eh ana amasiye
angazopeni monga ana anunso
angazopeni monga ana anunso wosataya
angazopeni ye monga, ana anunso
angazopeni ye monga, ana anunso
[verse 5]
chifundo, ndili chifundo ine
chifundo, ndili chifundo ine
mavhuto, ndili mavhuto ine
mavhuto, ndili mavhuto ine
amai anandilela
anamwalila kale
amai anandilela ine anamwalila kale
poenda ndimangolila
kuk*mbuka ondibala
poenda ndimangolila ine
kuk*mbuka ondibala pogona
ndimisozi chabe
bambo anga muli kuti inu
pogona ndimisozi chabe
bambo anga muli kuti inu
ndakulila muumpawi
wopatsa chisoni ndithu
ndakulila muumpawi
wopatsa chisoni ndithu
ngati muli ndiumoyo
kapena munamwalila, ngati muli ndiumoyo
kapena munamwalila
bwanji osabwela kutulo, kapena ndingakondeleko
bwanji osabwela kutulo, kapena ndingakondeleko
chifundo
ndili chifundo ine
chifundo, ndili chifundo ine
mavhuto, ndili mavhuto ine
mavhuto, ndili mavhuto ine
Random Song Lyrics :
- sonha alice - charruh lyrics
- down - jaye madison lyrics
- medicine - shrunko lyrics
- menace - hodgepodge lyrics
- coma breath - 404 guild lyrics
- awakening - despite (death metal) lyrics
- percs - kiid spyro lyrics
- shoot your shot - ca$htalk lyrics
- takni me takni - ludi konj lyrics
- all the time (voice memo) - sean kennedy lyrics