lirikcinta.com
a b c d e f g h i j k l m n o p q r s t u v w x y z 0 1 2 3 4 5 6 7 8 9 #

diso - arc nthambi lyrics

Loading...

(verse 1)
nkhani zanga mumakamba ,luso langa kuliyika mmasamba
kundiweta ngati mpaka mw*ngodziwa ndine mkango kuyamba kusaka
mwanditokosa k*mpanga ndingobwera ndikuthyola mipaliro kuchotsa mitu ndizikhaliro
i’m running in the city mucairo
muwuni ndi nyali zinalipo timangodikira match
moyo phw*nga ndichi dance flow
kuwutengera ma heart break
poyamba ankangodutsa pano akuti zima “hie bro”
ayi bro. ankandiponya ma stones,kuwumbuza zima stonzi

(bridge 1)
sometimes i stay quiet kuk*mbukira zomwe ndawona ma back days
poshala ndimati anzanga ,k*mpasa kwawo mipeni
all days are not sunday, it’s my time now ndiwale eeh eh

(verse 2)
ndafuwula mokweza kugumula linga lomwe munayikalo
ndabwera ndimalawi a moto uwotsa minga zomwe munayikazo
tinali tisanayambe tangoyamba pano ndinu ma follower
mesa munatitulika mwaima pakh0m* nkuyamba kukugogodanso
nde ndine man
nduvaya straight sindikuyenda m’mbali
i got the vision
i’ve gotta bigger plans
i burn it down
ndayaka man
i will never fall down
amafuna kulanda mpando w*nga man
ndikukang’anthani , i’m a king mafana gwadani panopa zopusa ndimakana
(bridge 2)
ndangobwera ndizikwanjе
mafana opusa onse afe
kuchotsa mitu ndi uwendе
usayese kudhoja umva pain pain
ndinthawi yanga ndikukantheni yeah yah aaa

(verse 3)
mafana nkabwera mukhala pansi
smashing the plates mudyera pansi
mukhalebe chete ndikupalasani
yeah i’m a fledy ndikusalazani
i’m proud of my ghetto,they show me love
working hard that’s why i’m going high
kudikirira nyengo zanga man heh

(bridge 3)
ndili pa eazy ndinabwera
tcheda ndingotenga
mumaseka now i’m way up
ndili pa eazy ndinabwera
tcheda ndingotenga
mumaseka now i’m way up
nkhawa zanga zonse zatha now
see i keep on shining now
nkhawa zanga zonse zatha now
see i keep on shining now

Random Song Lyrics :

Popular

Loading...