pa chibendo - bishop 1800 lyrics
yeahhhhh
ngati unafila utabwela pacribento panga
ubwele tizapangeso
up town mommy koma akuti ali mbali yanga
ngakhale ndili mfana wamughetto
amakonda kunena kuti ndimapanga zamatama
sindiyankha ma text tikasiyana
siine mwana
ubwele ubwele pa bendo
eh uziwa kale uzandipeza ndikutrapper
sindikunama sindima capper
olo ntachezela ku worker usiku wonse masana ndimapitilizabe work sindima napper
uzingonena zomwe ufuna usamabite bout the bush
as for me i’m a simple guy ndimagifuna ndimwe ndidye ndiwinje pakhale ma kush
kungondichotsele zimenezo ndekuti wandisokoneza lingual
kungolakwitsa chimodzi ndеkuti ukhala single
anchina ready to mingle
timamulowa boyfriеnd wake akablunder
nkazi wabho sakhala yekha timalanda
ngati unafila utabwela pacribento panga
ubwele tizapangeso
up town mommy koma akuti ali mbali yanga
ngakhale ndili mfana wamughetto
amakonda kunena kuti ndimapanga zamatama
sindiyankha ma text tikasiyana
siine mwana
ubwele ubwele pa bendo
ati famous kodi mesa ndiwe duntu
nde bwanji katundu choncho ndiwatunthu
kurunner madancehall ngati mafumu
ndipeze mu 25 ndili mu hood
i’m b*lls deep in that p*$$y
i’m checking the anatomy
i beat up like the f*ck
men i swear she don’t f*ck for free
she asking when she gon be my wife i said chill
she saying that i’ve been inducted for this bill
ngati unafila utabwela pacribento panga
ubwele tizapangeso
up town mommy koma akuti ali mbali yanga
ngakhale ndili mfana wamughetto
amakonda kunena kuti ndimapanga zamatama
sindiyankha ma text tikasiyana
siine mwana
ubwele ubwele pa bendo
eh uziwa kale uzandipeza ndikutrapper
sindikunama sindima capper
olo ntachezela ku worker usiku wonse masana ndimapitilizabe work sindima napper
ngati unafila utabwela pacribento panga
ubwele tizapangeso
up town mommy koma akuti ali mbali yanga
ngakhale ndili mfana wamughetto
amakonda kunena kuti ndimapanga zamatama
sindiyankha ma text tikasiyana
siine mwana
ubwele ubwele pa bendo
Random Song Lyrics :
- encontro das águas - the rebel (ita) lyrics
- d.t.f. - menya lyrics
- sink the ship - love cry (usa) lyrics
- bring back trump - roadrun cmoe & yung hood lyrics
- all in fun - steve lawrence & eydie gorme lyrics
- surprise - girl of god lyrics
- come back baby - the lagoons lyrics
- imagination high (hi5 remix) - lucas valiante & hi-5 lyrics
- kamikaze - of monsters and men lyrics
- nothing left - vesliah lyrics