
wakuba (interlude) - crispy malawi & dirty flo lyrics
[intro: dirty flo]
aku recorder ndi yashie
iwe aku recorder ndi yashie
iwe aku recoder ndi yashie
[pre*chorus: crispy malawi, dirty flo, both]
wakuba
amawoneka woyera koma ndi mkazi wakuda (eh)
mkazi wak*mpanda koma looks ndipanja wakunja (yea)
olo k*muloleza amatenga mwakuba
koma ali safe ali m’manja mwakuba
[chorus: dirty flo, dirty flow & crispy malawi]
uyo, uyo, uyo, uyo, wakuba
uyo, uyo, uyo, uyo, wakuba
uyo, uyo, uyo, uyo, wakuba
uyo, uyo, uyo, uyo, wakuba
uyo, uyo, uyo, uyo, wakuba
[verse: crispy malawi & dirty flo]
k*mu caller dirty ati iyeyo ali kwa duda
kuyithoka boys yanga ati samasuta
koma amazanditenga kuvaya kwa plug koma kusonkha yamafuta
ndimadya ndine koma kungoti ghetto simakhuta
malo si ake koma ndadabwa wamasuka
attention yanga sinduyiwona ndani wasunga? (yeah)
atha kubela mpweya iwe ndikubanika
ofunika k*mu searcher uyu akamapita (mh)
(yeah, yeah) nde akamavina mpamene umaziwa kuti ass yangodzadza ndi ma fats
amangokwiya ati ndimachulutsa ma facts
pa tiktok ndimafila f*kwa ali ndi chi nyash
olo mbina ndamudabwa mene wanyamulira
waba uku koma uku nkomwe wajudukira
timuphika f*kwa watibela chopakulira
waba moto fanzi ikuwona ngati wazimitsira
[pre*chorus: crispy malawi, dirty flo, both]
wakuba
amawoneka woyera koma ndi mkazi wakuda (eh)
mkazi wak*mpanda koma looks ndipanja wakunja (yea)
olo k*muloleza amatenga mwakuba
koma ali safe ali m’manja mwakuba
[chorus: dirty flo, dirty flow & crispy malawi]
uyo, uyo, uyo, uyo, wakuba
uyo, uyo, uyo, uyo, wakuba
uyo, uyo, uyo, uyo, wakuba
uyo, uyo, uyo, uyo, wakuba
uyo, uyo, uyo, uyo, wakuba
Random Song Lyrics :
- come pree - leuca lyrics
- west of the fields - live from rock city, nottingham / 1984 - r.e.m. lyrics
- mr. nice guy - acting lovers lyrics
- dym - czachukozak lyrics
- depressions - vita ohne li lyrics
- give five (british version) - hi5 uk lyrics
- soldier on! - megadeth lyrics
- seat at the table - common hymnal, sharon irving & vincent charlow lyrics
- anne - dion warlocke lyrics
- verset de br - bulk requiem lyrics