
album otw - crispy malawi lyrics
[intro]
ndisanene f*ck buddy
company sindingapange
ndisanene f*ck buddy
company sindingapange
[chorus]
wandiuza wandisowa ndati ineso
koma ndi ineso sitingabweleranso
anzako umawauza umkandikonda ineso
koma ndi iweso sinding*yambileso
koma ndisaname
mwina titha kungokhala ma f*ck buddies
utha k*mandikhola ukafuna company
koma zobwelerana nde singapange
[verse 1]
ndiku dropa tape 2 koma album ili on the way
ndungofuna ndingolowa chaku nkhatabay or capemaclear and put my phone away
i don’t know how, buh i know i will find a way
nde tandipase plan kuti ti linky
or ndingovunga location kuti ufike
ndukuvaisa ku kitchen kuti uphike
kenako ukuziwa kale kuti ufile
kuvayisa pa bar kut u sippy
kuikora nyimbo kuti uvine
fe fr fr fr kuti ununkhile
zaza wezi brain izungulire
kwinako ukuziwa kale zoti uchite
nde tasekeleratu usandilusire
wabwera utatchena koma tandivulire
another round ima kaye ndikusutire
Random Song Lyrics :
- adam (act like) - fred again.. lyrics
- pain - n3wport lyrics
- sweet - doou$hii lyrics
- bad news - treistemm lyrics
- busy boy - chloe x halle lyrics
- e.j.e. - epis dym knf lyrics
- βράδια αξημέρωτα (bradia akshmerwta) - solmeister lyrics
- waiting on bad news - the tourist company lyrics
- greg - big midas lyrics
- sokakta kim var - veyasin lyrics