
angobwerabe - crispy malawi lyrics
[intro]
f*f9ine
[pre*chorus]
ma babe ambiri man angobwerabe
43, chimaliro , nyambadwe
ena ali single ena umake
ali ndi a eniake
ali single ngati ali ku party
[chorus]
ali single ngati ali ku party
akufila ati tik*mane
sitik*mvana ngati sitingadyane
ofila dancehall sangamanyade
[verse 1]
nnamukwera kale sanganditsike
ati ali ndi guy oti sangamu cheaty
ex w*nga wina anagwidwa ndi dj
koma ntafuna nditha k*mu caller kuti ndimu*
k*mudeleter ngati amangooneka bho pa ma pictures
ama roller ndi adani k*mawauza kuti andidisse
nnangoziwa kuti si level basi k*mandipanga compare ineyo ndi achina piksy
iwe, yachina spe ndi 1 of 1 sungamafananize
sindingakunamize, ngati sufila dancehal sindingakukakamize
nditha kushala nawe koma sindingakhalitse
umuuzenso blesser wako ndikugulisa ma lipha ndi ma t shirt
osamaphwеkesa mission
[pre*chorus]
ma babe ambiri man angobwerabе
43, chimaliro , nyambadwe
ena ali single ena umake
ali ndi a eniake
ali single ngati ali ku party
[chorus]
ali single ngati ali ku party
akufila ati tik*mane
sitik*mvana ngati sitingadyane
ofila dancehall sangamanyade
Random Song Lyrics :
- roseira - ana muller lyrics
- si tú saltas - aaron lyrics
- november - tyler, the creator lyrics
- selo das promessas - roberta di angellis lyrics
- torn between two lovers - 劉美君 feat. gin lee lyrics
- eu to de olho - lucero lyrics
- vulcano (radio edit) - francesca michielin lyrics
- paradigm - slum sociable lyrics
- back for more - justine skye lyrics
- love me now - db feat. michel le fleur lyrics