ayi zikomo - crispy malawi lyrics
[intro]
malawian
ayi zikomo
[chorus]
kudzuka mornaz kugwada pansi kuthokoza jah, jah f*kwa leronso ndadzuka ndi moyo
gratitude is a must ndimawinner ndikangodzuka sindimgaphwekese
ayi zikomo, ayi zikomo
yeah, ayi zikomo
[verse]
sorry ngati zili zapa easy kwa iweyo
kwa ifeyo ndiza hard takulira mu zikh0m*
kwachoka nzako pali malo ngati suk*mvesa ndekuti sunabholeko za after domo
ndimayenda ndi gang koma nditha kuyenda ndekha
ngati pomwe pali abalepo adani ali pomwepo
eish, funa imali wamva? ngati zili zosakhudza cash
zisandikhudze ndakana nono
dollar ya show sikukwana koma umakwana
no thanks, i can’t take the offer, ayi zikomo
i can’t show up at your place f*kwa ukufila ngati aliyense akuyenera ashale konko
mamva zomwe mandi mandinena ndimafuna kuyankha
koma ndikango burner ndimangoti (ayi zikomo)
[chorus]
kudzuka mornaz kugwada pansi kuthokoza jah, jah f*kwa leronso ndadzuka ndi moyo
gratitude is a must ndimawinner ndikangodzuka sindimgaphwekese
ayi zikomo, ayi zikomo
yeah, ayi zikomo
[outro]
zikomo, zikomo, ayi zikomo
Random Song Lyrics :
- how can i forget - bright visions & rogue zero lyrics
- hatodik érzék - franko (hu) lyrics
- лирика (fin 2) - white siemens lyrics
- ты знаешь (you know) - qwemouzo lyrics
- todo va a mejor - drastar lyrics
- maalish - معلش - tamer hosny - تامر حسني lyrics
- break through - samuel j lyrics
- kingdom - darrell cole lyrics
- lean speaks from heaven (outro) - razg69 lyrics
- на "у" (on "u") - лёва twice (swagga music) lyrics