
choncho - crispy malawi lyrics
[chorus]
olo no make up ukuoneka bwino choncho
umandiwaza ukamaoneka choncho
umandiwaza uka dressa choncho
unandikomzekera choncho
unapanga ubale wamadzi ndi soap
uyambe ku fire ukubweza moto
international siza local
digital maskini wavaya global
[verse 1]
wandipasa phone number nzake ali pompp
ndukuuza sungagwire ngati ulibe khodo
akufila fragrance,freckled mo nnda mixa ndi torm ford
ngati ukufuna utha ku halla nimangomemya phone call
what’s up with your t shirt?
ulibe abale kapena knq
ndaonela skirt yonga’amba kuti palibe akuku soka
ndi mfana ozimva or akasiya ku talka
akakwiya amandi blocker
akamapita ndimamukoka
[chorus]
olo no make up ukuoneka bwino choncho
umandiwaza ukamaoneka choncho
umandiwaza uka dressa choncho
unandikomzekera choncho
unapanga ubale wamadzi ndi soap
uyambe ku fire ukubweza moto
international siza local
digital maskini wavaya global
[verse 2]
choncho nde uziti sumandifila choncho
munthu umangofuna komwe ndiliko ukhale komko
ndi nthawi yanga ona nthawi ikuti spe o’clock
siwe snack ndiwe full meal tipase mpeni ndi fork
huh
beef kudya ndekha
pa level nditadekha
movie tiku major
mix kamangoseka
ex wake akulenga
uli ndi mfana otentha
zinamupeta§zinamutembenuza
anatumiza leka
[chorus]
olo no make up ukuoneka bwino choncho
umandiwaza ukamaoneka choncho
umandiwaza uka dressa choncho
unandikomzekera choncho
unapanga ubale wamadzi ndi soap
uyambe ku fire ukubweza moto
international siza local
digital maskini wavaya global
Random Song Lyrics :
- a street called straight - renaldo & the loaf lyrics
- sulla luna - joe tossini lyrics
- free the 4 - twelve'len lyrics
- champion at keeping them rolling - the dubliners lyrics
- sanat - värttinä lyrics
- you - mikey100k lyrics
- auf meinen schultern - tomte lyrics
- nøthing - nø_øne lyrics
- fourninesix - swizz lyrics
- if you love me - steven page lyrics