komaliza - crispy malawi lyrics
it’s nyce, f9ine entertainment
i know, i know, i know, i know
kuti kakhala (komaliza)
ayayayaya (malawian), mmh
[chorus]
umangowona kundinyaditsa (komaliza) (aah ah)
ndine amene ndima kukwanitsa (komaliza) (aah ah)
ngati zathapo chabwino komaliza (komaliza) (aah ah)
ndipatse chance komaliza (komaliza) (aah ah)
chabwino ndingogunditsa (komaliza) (aah ah)
ati spe “bwanji umandivutitsa” (komaliza) (aah ah)
“ndikakulola basi uzindipusitsa” (komaliza) (aah ah)
“ukandihuga basi uzindikissa” (komaliza) (aah ah)
“koma money tima babe ena uk*mawa hitter” (komaliza) (aah ah)
haa eh chabwino basi ndasiya (komaliza) (aah ah)
mangofuna ukastresser uzili njanjitsa (komaliza) (aah ah)
ndilipa top pamwamba pakopa sinditsika (komaliza) (aah ah)
ndimadana ndi zondipusitsa (komaliza) (aah ah)
[verse]
bwanji? uli ndi ine olo pa msika?
ndiwe mtengo nditha kukwera ndi kutsika
ndamenya shot kuti nkhani ndingozifupikitsa
round one, two titha k*menya molumikiza
[chorus]
umangowona kundinyaditsa (komaliza) (aah ah)
ndine amene ndima kukwanitsa (komaliza) (aah ah)
ngati zathapo chabwino komaliza (komaliza) (aah ah)
ndipatse chance komaliza (komaliza) (aah ah)
chabwino ndingogunditsa (komaliza) (aah ah)
ati spe “bwanji umandivutitsa” (komaliza) (aah ah)
“ndikakulola basi uzindipusitsa” (komaliza) (aah ah)
“ukandihuga basi uzindikissa” (komaliza) (aah ah)
“koma money tima babe ena uk*mawa hitter” (komaliza) (aah ah)
eh chabwino basi ndasiya (komaliza) (aah ah) (siya) (siya)
mangofuna ukastresser uzili njanjitsa (komaliza) (aah ah)
ndilipa top pamwamba pakopa sinditsika (komaliza) (aah ah)
ndimadana ndi zondipusitsa (komaliza) (aah ah)
[outro]
(komaliza), komaliza
komaliza
komaliza
Random Song Lyrics :
- ne20 (intro) - neurosatan lyrics
- zyzz - mizulx & bleach mane lyrics
- morning light [remix] - уикэнд (wkknd) lyrics
- what you doing - chris clark lyrics
- en boucle - sadek lyrics
- one to one - the passage (uk) lyrics
- suflet pereche - neli thgod lyrics
- watanabe - douze déluge lyrics
- top or cliff - kim sejeong (김세정) lyrics
- med change - michael motorcycle lyrics