
step by step (audiomack version) - crispy malawi lyrics
[intro]
malawian
yeah
hmmmm
[chorus]
step by step tikukwera
wekha ukuona kuti tikupanga elevate
ma guy nde asankha kuti azifila spe
ena nde ena akuopa akupanga hate
sleepless nights sakugona
sapezeke pa poster aka runner tings sitingamupeze[?]
m*th* k*ma hater koma sungadiletse
m*th* k*ma hater koma sungandiletse
[verse]
fresh and clean pa chi corner
k*mata pa poster show yo runner ndekha
homeboy tsitsi w*ngopota
tonse tangotchena nde ena akuti tikupenga
ndine one of a kind ngati ganja
iweyo tangodekha olo abwеre ndi yolenga
aliyesе apa anayamba yekha
sitinayambile limodzi ngati liwiro lamu mchenga[?]
mhu
from zigege to tacos
ndichi fine mamie ngati riana bagus
ndinayambira kusuta mibongo
pano one par yokha imazunguza ubongo
one par itha kukuzunguza ubongo
one par yokha ima zazunguza ubongo
one par yokha itha kuku zunguza ubongo
one par yokha itha kuzu…mhu wamva?
[chorus]
step by step tikukwera
wekha ukuona kuti tikupanga elevate
ma guy nde asankha kuti azifila spe
ena nde ena akuopa akupanga hate
sleepless nights sakugona
sapezeke pa poster aka runner tings sitingamupeze[?]
m*th* k*ma hater koma sungadiletse
m*th* k*ma hater koma sungandiletse
[outro]
m*th* k*ma hater koma sungadiletse
m*th* k*ma hater koma sungandiletse
Random Song Lyrics :
- trappers & steppin - baby jamo lyrics
- mikelenjelo - patron lyrics
- é o jogo - sumano lyrics
- ангел (angel) - злой дух (zloy duh) (rus) lyrics
- out of service - sydney rose lyrics
- cowpunk - scott goddard lyrics
- bad guy - the keeng lyrics
- couch days - backyard (backyard universe) lyrics
- breaking bad - karin duff lyrics
- kentucky flood - josiah and the bonnevilles lyrics