
why - eli njuchi lyrics
[verse 1]
ndi yama*hope
ndalimba mtima lero sangie
sindikudziwa zitha bwanji?
sumandiyankha pa facebook, insta, twitter nanji
ma bluetick onswewa bwanji?
i’ve been following you mayi wa ngwiro
kuyambira form 1 mpaka 4
every show ndimakhala konko, sindinajombeko
sangie, ukundithela bundle
[chorus]
kapena mwina chif*kwa ndine mwana? sangie
sizikugwirizana, sangie
mesa tidzikondana
ndiyankhe njuchi akukakamire
tell me why?
tell me why?
tell me why?
ndiyankhe njuchi akukakamire
tell me why?
tell me why?
tell me why?
ndiyankhe njuchi akukakamire
[verse 2]
tikak*mana kwa sispence
all i get ndi aire basi
sangafile njuchi alibe viwiе
akatha mtunda ndi minibus
ndikati ndipemphe selfiе uli busy
ndikhole number ili busy
ayi busy
still i do it all for love
ndiyankhe njuchi aku*, uh
[chorus]
kapena mwina chif*kwa ndine mwana? sangie
sizikugwirizana, sangie
mesa tidzikondana
ndiyankhe njuchi akukakamire
tell me why?
tell me why?
tell me why?
ndiyankhe njuchi akukakamire
tell me why?
tell me why?
tell me why?
ndiyankhe njuchi akukakamire
tell me why?
tell me why?
tell me why?
ndiyankhe njuchi akukakamire
tell me why?
tell me why?
tell me why?
ndiyankhe njuchi akukakamire
Random Song Lyrics :
- vi vinner! - dom viktiga skorna lyrics
- go.fuck.yourself - expain lyrics
- fill it up - krimelife ca$ lyrics
- rebirth - atlantis awaits lyrics
- i hate that... - jerome lyrics
- brother - peter katz lyrics
- had to have him - damhnait doyle lyrics
- give dem - frenna lyrics
- cover me up - rodney atkins lyrics
- tetris (spanish remix) - tazmatik lyrics