
ali dere - faith mussa lyrics
Loading...
[chorus]
ali dere
ali dere uyu
ali dere nkulinga iwe uzayenda naye
ndiwotere, amatere uyu
ali dere nkulinga iwe uzayenda naye
ali dere
ali dere uyu
ali dere nkulinga iwe uzayenda naye
ndiwothere, amatere uyu
ali dere nkulinga iwe uzayenda naye
[refrain]
well try to know me better,before you talk about mе
[verse]
ali dere
nthawi zina umati ndine wabwino
nanga lеro bwanji ukuti ndine woyipa?
koma ine ndiwe sitinak*manepo?
koma ine ndiwe sitinachezepo?
[refrain]
well try to know me better,before you talk about me
[chorus]
ali dere
ali dere uyu
ali dere nkulinga iwe uzayenda naye
ndiwotere, amatere uyu
ali dere nkulinga iwe uzayenda naye
ali dere
ali dere uyuyu
ndiwotere uyuyu
Random Song Lyrics :
- magnam odium - hxnjv lyrics
- ain't talkin' 'bout love - toto lyrics
- breed to death (xian "feed" antkow remix) - dismantled lyrics
- 13 atslēgas vārdi - armands lyrics
- all love - michael millions lyrics
- unbearable - the wonder stuff lyrics
- oblio - fuckthepain lyrics
- swamp thing - hiatus kaiyote lyrics
- thraxx etiquette - lil tracy lyrics
- world without you - judie tzuke lyrics