lirikcinta.com
a b c d e f g h i j k l m n o p q r s t u v w x y z 0 1 2 3 4 5 6 7 8 9 #

aphiri - faith mussa lyrics

Loading...

[verse 1]
a phiri anabwera kuchoka ku harare
a phiri anabwera kuchoka ku harare
pobwera k*meneko anabwera ndi suitcase
pobwera k*meneko anabwera ndi suitcase
koma mkati mwa suitcase munalibe kanthu shuwa
ndati mkati mwa suitcase munalibe kanthu shuwa

[pre*chorus]
a phiri anaganiza “kodi ndidzayenda kuti?”
makolo anga onse anamwalira ku dara
a phiri anaganiza “kodi ndidzayenda kuti?”
makolo anga onse anamwalira ku dara
koma mkati mwa suitcase munalibe kanthu shuwa
ndati mkati mwa suitcase munalibe kanthu shuwa
a phiri anaganiza “kodi ndizayenda kuti?”
makolo anga onse anamwalira ku dara
a phiri anaganiza “kodi ndizayenda kuti?”
makolo anga onse anamwalira ku dara

[chorus]
a phiri eh
a phiri eh
a phiri eh
a phiri eh
a phiri eh
a phiri eh
a phiri eh
a phiri eh
a phiri eh
[pre*chorus]
a phiri anaganiza “kodi ndizayenda kuti?
a phiri anaganiza “kodi ndizayenda kuti?
ndati phiri anaganiza “kodi ndizayenda kuti?
koma mkati mwa suitcase munalibe kanthu shuwa

[chorus]
a phiri eh
a phiri eh
a phiri eh
a phiri eh
a phiri eh
a phiri eh

Random Song Lyrics :

Popular

Loading...