akondakitale - gwamba lyrics
[intro: lawi]
yi, aye*iye*yah
aye*iye*yah
[chorus: lawi]
akondakitale ndalama ndalipilayi ndati ndipemphe, mundibwenzereko chenje

ulendo w*nga ukathera ku lilongwe, m’deport
koma ndipemphe, mundibwenzereko chenje
inu ulendo w*nga ukathera ku lilongwe, m’deport
koma ndipemphe, mundibwenzereko chenje, yi
[verse 1:gwamba]
aish, ndalama nde yavuta pa nyasa
daily fans k*mayisaka
sikuwona zoti ndiwe shasha
k*menya business basi k*mayitsatsa
nde mukapeza ka ndalama sister, chonde k*makagwiritsitsa
mukamagona nako kukafunditsa
kwachuluka mbava nde muzikabisa
[chorus: lawi]
yi, ndikupempha mundithandize
yi, w*ngondivuta ndi uphawi (ayi)
ah, ah
akondakitale ndalama ndalipilayi ndati ndipemphe, mundibwenzereko chenje
akondakitale ndalama ndalipilayi ndati ndipemphe, mundibwenzereko chenje
ulendo w*nga ukathera ku lilongwe, m’deport
koma ndipemphe, mundibwenzereko chenje
inu ulendo w*nga ukathera ku lilongwe, m’deport
koma ndipemphe, mundibwenzereko chenje, yi
[verse 2: gwamba]
aish, conductor pokwera umati 100 ndangokhala pansi ukuti 120
aseh, osaziyamba zin*z*
muno sindichoka ngati sundipatsa change
wekha ukudziwa dollar ili pa minga
povaya kudedza pena kukwera njinga
umayesa ngati ukundiyimba
lero lonkha wandilira sindiyimva
[chorus: lawi]
yi, ndikupempha mundithandize
yi, w*ngondivuta ndi uphawi (ayi)
ah, ah
akondakitale ndalama ndalipilayi ndati ndipemphe, mundibwenzereko chenje
akondakitale ndalama ndalipilayi ndati ndipemphe, mundibwenzereko chenje
ulendo w*nga ukathera ku lilongwe, m’deport
koma ndipemphe, mundibwenzereko chenje
inu ulendo w*nga ukathera ku lilongwe, m’deport
koma ndipemphe, mundibwenzereko chenje, yi
[verse 3: gwamba]
aish, komanso yesu akufuna change mama
koma change akufuna iye si ndalama
akufunitsitsa inuyo makamaka mutasintha ndikuyamba k*mutsata
mapemphero ndi hustle ya uzimu
mukapusa tsiku lomaliza, no change
mapemphero ndi hustle ya uzimu
ukapusa tsiku lomaliza, no change
[chorus: lawi]
yi, ndikupempha mundithandize
yi, w*ngondivuta ndi umphawi
ah, ah
akondakitale ndalama ndalipilayi ndati ndipemphe, mundibwenzereko chenje
akondakitale ndalama ndalipilayi ndati ndipemphe, mundibwenzereko chenje
ulendo w*nga ukathera ku lilongwe, m’deport
koma ndipemphe, mundibwenzereko change
inu ulendo w*nga ukathera ku lilongwe, m’deport
koma ndipemphe, mundibwenzereko chenje, yi
Random Song Lyrics :
- brickxbrick - advent lyrics
- grateful - the belief cycle lyrics
- lettere mancanti - u.g.o. lyrics
- baiji - ginjin lyrics
- конченный человек (goner) - guccihighwaters lyrics
- nur für den moment - payy lyrics
- spectral dusk - evening hymns lyrics
- apathetic whistle - fuel eater lyrics
- death to vegans - royce bennett lyrics
- een ander spoor - karen damen lyrics