
pang'ono - joe ikon lyrics
[intro]
ikon wafika, no id chinzika
ikon wafika (ayo billy), ikonini
ayi!
[verse 1]
dzulo ndimati mowa ndaleka, mowa ndaleka (ayi!)
leroli ndingofuna macheza
ndimati mowa ndaleka, mowa ndaleka
leroli ndangobwelera shisha
ndazazindikira kuti pondichera ndinamwa mwamacheza
koma mowa si madzi
ndazazindikira kuti pondichera ndinamwa mwamacheza
koma mowa si madzi
[chorus]
ndikati dj tangokweza pang’ono, ndingovina pang’ono
sindimasuka kwambiri ndingomwako uwiri, ay
ndungofuna pang’ono (oh)
sindimasuka kwambiri ndingomwako uwiri, ay
ndungofuna pang’ono
ndikati dj tangokweza pang’ono (kwambiri ayi), ndingovina pang’ono (pang’ono)
sindimasuka kwambiri ndingomwako uwiri, ay
ndungofuna pang’ono (kwambiri ayi)
sindimasuka kwambiri ndingomwako uwiri (pang’ono basi), ay
Random Song Lyrics :
- daisy - yung kiy ft oyin lyrics
- visionário - little kush lyrics
- down for you - micki jayy lyrics
- off-white - young rose lyrics
- trollz remix - maisnerd lyrics
- beeni - ckay lyrics
- sway with me (solo version) - galxara lyrics
- tchau tchau - devinho novaes lyrics
- walk & like - jon williams lyrics
- shrugs - juiceb☮x lyrics