lirikcinta.com
a b c d e f g h i j k l m n o p q r s t u v w x y z 0 1 2 3 4 5 6 7 8 9 #

zidutswa - kamarih lyrics

Loading...

mmh mmh mmh mmh mmh
come on yeah

i heard all about you
koma nd*nkayesa uzasintha ndi chikondi yeah
i just couldn’t face the truth
i chose to be blinded by your body

abale atandiletsa sind’amvere nd*nkayesa angopanga chabe nsanje
oh nsanje angopanga chabe nsanje
anzanga atandiletsa sind’amvere nd*nkayesa angofuna andilande
ah ndilande nd*nkayesa andilanda

pano w*ngosiya zidutswa
zidutswa m’mtima mw*nga
zidutswa m’mtima mw*nga
w*ngosiya zidutswa
zidutswa m’mtima mw*nga
waswa mtima w*nga yeah

no one left here to lean on
no one there to save me i’m going under
i chose you above it all
pano ndaphula zibwana zanga

abale atandiletsa sind’amvere nd*nkayesa angopanga chabe nsanje
oh nsanje angopanga chabe nsanje
anzanga atandiletsa sind’amvere nd*nkayesa angofuna andilande
ah ndilande nd*nkayesa andilanda
pano w*ngosiya zidutswa
zidutswa m’mtima mw*nga
zidutswa m’mtima mw*nga
w*ngosiya zidutswa
zidutswa m’mtima mw*nga
waswa mtima w*nga yeah

Random Song Lyrics :

Popular

Loading...