
ineyo - kwemogoon lyrics
[intro]
[?]
[chorus: kwemogoon & kingdolla]
kakuti kathozipha chif*kwa cha ineyo
geliso kusiya chif*kwa cha ineyo
kathawaso kwawo chif*kwa cha ineyo
kati kathobwera ku show chif*kwa cha ineyo
kakuti kathozipha chif*kwa cha ineyo
geliso kusiya chif*kwa cha ineyo
yeah*ah, kathawaso kwawo chif*kwa cha ineyo
kabwera ku show chif*kwa cha ineyo, yah
[verse 1: kwemogoon & _kingdolla_]
kak*ma talker zosezo, eh
panopa nde tapanga settle, eh
kulimba ntima ngati metal, eh
kufilitsana ngati tomato
kati kagoma nane ndikhale wake boo
ndikafuna ku trapper ndizikatenga ku stu’
tizapange tiana ka jessy ndi ka ju’
nde kamavunga emoji kundiyika mu mood
[chorus: kwemogoon & kingdolla]
kakuti kathozipha chif*kwa cha ineyo
geliso kusiya chif*kwa cha ineyo
kathawaso kwawo chif*kwa cha ineyo
kati kathobwera ku show chif*kwa cha ineyo
kakuti kathozipha chif*kwa cha ineyo
geliso kusiya chif*kwa cha ineyo
yeah*ah, kathawaso kwawo chif*kwa cha ineyo
kabwеra ku show chif*kwa cha ineyo, yah
[verse 2: kwemogoon & kingdolla]
she say she down for mе kathopanga chilichose (chili’, chili’)
olo ‘usiya geli bola ifeyo tikhale tose (eh, eh, eh, eh)
kamafila kwemo no lie
kamandiwuza ngamo each and everyday no lie (no lie)
kakuti sikangandisiye
kangofuna kukhala ndine
ndikamunda kafuna ndikalime
kabweleratu kati kazishala ndine
yah, yah, kangofila star
[chorus: kwemogoon & kingdolla]
kakuti kathozipha chif*kwa cha ineyo
geliso kusiya chif*kwa cha ineyo
kathawaso kwawo chif*kwa cha ineyo
kati kathobwera ku show chif*kwa cha ineyo
kakuti kathozipha chif*kwa cha ineyo
geliso kusiya chif*kwa cha ineyo
yeah*ah, kathawaso kwawo chif*kwa cha ineyo
kabwera ku show chif*kwa cha ineyo, yah
[outro: kwemogoon]
chif*kwa cha ineyo
chif*kwa cha ineyo
chif*kwa cha ineyo
Random Song Lyrics :
- hosting a soul - two years dead lyrics
- neon nights - marsupial soup lyrics
- princess power theme song - princess power lyrics
- cepheus - 2u_ukii lyrics
- feel the same - cxrpse lyrics
- christmas in july - swaine lyrics
- for the tears to come - moe bandy lyrics
- für immer - peat lyrics
- flower - trysail lyrics
- oko za oko, rym za ząb (demen remix) - smarki smark lyrics