
kape! - lil al lyrics
[intro]
yo 14 you got another one
ha, hahahaha
lil alzizizo
[chorus]
kape! sangacheze ndine
nchif*kwa zikuyenda ndipo sizingasimphine
sungadizadwe kusiphe, kofwala kuti ndilabwe ndimafunika ndilipidwe
iwe tangowona umene ndayika
tangowona umene ndayika
sungandipose kutchena mukupepuka mafana muk*manyika
huh iwe, iwe tangowona umene ndayika
[verse 1]
belo sh*t ndungoweneka za mtika
ngati ndimamvana ndi rose wabho bho
koma ndi wa cash drip
kungofika pa malo aliyense akufuna andimenyetse sip
tungodripper wa mame sungatipeze tik*menya ma nip
zi ana zuziwa i’m him zungofuna zindidyetse lip
ndungokakisser nipple kenako ndikadye nipla
umaziwa yanga ija sindiphweketsa limbwa
[chorus]
kape! sangacheze ndine
nchif*kwa zikuyenda ndipo sizingasimphine
sungadizadwe kusiphe, kofwala kuti ndilabwe ndimafunika ndilipidwe
iwe tangowona umene ndayika
tangowona umene ndayika
sungandipose kutchena mukupepuka mafana muk*manyika
huh iwe, iwe tangowona umene ndayika
[verse 2]
nda dropper kwambiri ma guy mu game akubanika
ma trapper a ulesi onse nde ndik*maliza
ngati ulibe dollar ndiwe artist wokanika
feature price ndima charger ngati ndikukaniza (yeah, yeah)
anandi b*tcherko kale nde sindimgawatenge serious
kungomubweleka rack munthu wayamba kusanduka mysterious
ha k*machenjera ma kape atha kubela
atandi slima phone ndinawoneka ngati mfana wopepera
but i didn’t care mix ndinali mu club, chi mwana chimandigwedezera
kenako chikundinong’oneza “big slime ndimaku hopera”
ukamuuza boyfriend wanyuowani atakudyera mkaladi
[chorus]
kape! sangacheze ndine
nchif*kwa zikuyenda ndipo sizingasimphine
sungadizadwe kusiphe, kofwala kuti ndilabwe ndimafunika ndilipidwe
iwe tangowona umene ndayika
tangowona umene ndayika
sungandipose kutchena mukupepuka mafana muk*manyika
huh iwe, iwe tangowona umene ndayika
Random Song Lyrics :
- trumna - mlodydemon9 lyrics
- coffee time - frée lyrics
- cannibal - a.s.s.p. lyrics
- nódoas negras - pikapau lyrics
- bilmiyorum freestyle - kural lyrics
- diamond heart - big sky lyrics
- hoa đêm - quân bùi lyrics
- leave it on the line - teddy grossman lyrics
- out on my own - ni$h!th lyrics
- hell no - space lyrics