lirikcinta.com
a b c d e f g h i j k l m n o p q r s t u v w x y z 0 1 2 3 4 5 6 7 8 9 #

anafera chiboda - madalitso band lyrics

Loading...

[intro]
ine, ako
ine, ako
ine, ako
ine, ako

[chorus]
anafera chiyani kodi? anfera chiboda
anafera chiyani mayi? anfera chiboda
anafera chiyani kodi? anfera chiboda
anafera chiyani khaze? anafera chiboda
ena si awo? anafera chiboda
ena si awo? anafera chiboda
tawona, anafera chiboda
anfera chiyani kodi? anafera chiboda

[verse 1]
p*n*li mtsikana wina
p*n*li mtsikana wina
amene ankafuna banja
amene ankafuna banja
ati mamuna amukwatire
ati mamuna amukwatire
koma kamunayo akhale wachuma
koma kamunayo akhale wachuma
k*makana amuna osauka
k*makana amuna osauka
wayiwala banja si chuma
banja ku khumudwitsana
[pre*chorus]
ine, ako
ine, ako
ine, ako

[chorus]
anafera chiyani kodi? anfera chiboda
anafera chiyani mayi? anfera chiboda
anafera chiyani kodi? anfera chiboda
anafera chiyani khaze? anafera chiboda
ena si awo? anafera chiboda
ena si awo? anafera chiboda
tawona, anafera chiboda
anfera chiyani kodi? anafеra chiboda

[break: guitar solo]

[chorus]
anafera chiyani kodi? anfera chiboda
anafera chiyani mayi? anfеra chiboda
anafera chiyani kodi? anfera chiboda
anafera chiyani khaze? anafera chiboda
ena si awo? anafera chiboda
ena si awo? anafera chiboda
tawona, anafera chiboda
anfera chiyani kodi? anafera chiboda

Random Song Lyrics :

Popular

Loading...