
princess wanga - madalitso band lyrics
Loading...
tiya, tiya iwe tiya ndimakukonda
tiya, tiya iwe tiya ndimakukonda
tiya, tiya iwe tiya ndimakukonda
tiya, tiya iwe tiya ndimakukonda
hehe! ndiwe wekha wokondedwa w*nga, palibeso wina
tiya, tiya iwe tiya ndimakukonda
tiya, tiya iwe tiya ndimakukonda
tiya, tiya iwe tiya ndimakukonda
tiya, tiya iwe tiya ndimakukonda
[interlude: patrick thim sam]
chonde ndimakudalira iweyo sweetheart w*nga
ndiweyo wekha basi
osazandikhumudwitsa iyayi
wachikondi wapamba ndiweyo wekha basi
ndikamakhala ndimadalira iweyo wekha basi
tiya, tiya iwe tiya ndimakukonda
tiya, tiya iwe tiya ndimakukonda
tiya, tiya iwe tiya ndimakukonda
Random Song Lyrics :
- clouds (2010 version) - imagine dragons lyrics
- mikä on kun ei taidot riitä? - martti servo & napander lyrics
- leah - amariemowatt lyrics
- clean up man - creature fear lyrics
- pushing the clouds away - the san sebastian strings lyrics
- why wait - dj standout lyrics
- #41 - live from scranton - dave matthews band lyrics
- moments suspendus - chiens de paille lyrics
- prey hey - biffy clyro lyrics
- ball of confusion - hiltlesssword lyrics