
kumpeta milombe - mufrika lyrics
ooh ku mpeta milombe
kwathela ayamata ooh
ku mpeta milombe
kwathela alumbwana
ooh ku mpeta milombe
kwathela ayamata ooh
ku mpeta milombe
kwathela alumbwana
kuzebenza tisebenza bwino
ndalama timapeza
koma potsilizira pake eeh!
tinali nao anzathu
tinali kuseka nao
tinali nao astikana
odsziba kusamba bwino
nanga lelo alikuti
ambuye mwatisiyiranji
ooh ku mpeta milombe
kwathela ayamata ooh
ku mpeta milombe
kwsila alumbwana
ooh ku mpeta milombe
kwathela ayamata ooh
ku mpeta milombe
kwasila alumbwana
iyi nthenda niyoipa
ndiponso siyimasankha
imagwira aliyense
kuyambira kubana mpaka makolo
koma anyamata ndi astikana
nibame bakula maningi
nangatu tizakhala bwanji
popeza ndiye tsogoro
ooh ku mpeta milombe
kwathela ayamata ooh
ku mpeta milombe
kwathela alumbwana
ooh ku mpeta milombe
kwathela ayamata ooh
ku mpeta milombe
kwathela alumbwana
Random Song Lyrics :
- interpol - médine lyrics
- blood - kwik baztard yitz lyrics
- lifetime membership - dj premier lyrics
- de fiesta - conjunto atardecer lyrics
- rock with you - seu jorge lyrics
- #that power (i'm alive) - #that power lyrics
- no romeo - ethics lyrics
- que la suba pa' arriba - julion alvarez y su norteno banda lyrics
- knock shit - kossisko lyrics
- tower of sadness - k-rino lyrics