
panado - onesimus (mw) lyrics
[intro]
panado, panado, mm, mm
ma headache yeah, mm, mm
panado, panado, mm, mm
[verse 1]
amakonda miseche
amakonda munthu azivutika
zochitika ngati siwopemphera
daily, daily busy ntopoli
kubaya ma damage
kuwupatsa moyo w*nga challenge
machitidwe awo ngati judas
makhalidwe awo ngati njenjete
[pre*chorus]
amafuna ndikokoloke
amakhumbira nditapokoloka
amafuna ndisokoloke
amafuna mwina nditakomoka
amafuna ndikokoloke
amakhumbira nditapokoloka
amafuna ndisokoloke
amafuna mwina nditakomoka
[chorus]
ndi nsanje apatseni panado, panado
panado, panado
amweko panado, panado
panado, panado (yeah, yeah)
[post*chorus]
munthu wakula ndi nsanje
kaduka ndi nsanje
kaduka mwina ndi nsanje
kaduka, mtima wa chigawenga
munthu wakula ndi nsanje
kaduka ndi nsanje
kaduka ndi nsanje
kaduka, mtima wa chigawenga
[verse 2]
samafuna ndiyendere njale
samakondwa ndikamadya money
zikandiyendera amakoka chibale
zikamandivuta andinyoza k*mbali
koma mulungu wandichita balance, i relax
amamenya nkhondo nditakhala pansi
adani onse alemba m’madzi
samakondwa nane
[pre*chorus]
amafuna ndikokoloke
amakhumbira nditapokoloka
amafuna ndisokoloke
amafuna mwina nditakomoka
amafuna ndikokoloke
amakhumbira nditapokoloka
amafuna ndisokoloke
amafuna mwina nditakomoka
[chorus]
ndi nsanje apatseni panado, panado
panado, panado
amweko panado, panado
panado, panado (yeah, yeah)
[post*chorus]
munthu wakula ndi nsanje
kaduka ndi nsanje
kaduka mwina ndi nsanje
kaduka, mtima wa chigawenga
munthu wakula ndi nsanje
kaduka ndi nsanje
kaduka ndi nsanje
kaduka, mtima wa chigawenga
[outro]
panado, panado
ma headache, yah
ma headache, yah
panado, panado
ma headache, yah
ma headache, yah
ma headache, ma headache, yah
panado
panado
panado
panado, panado
panado
panado
panado, panado
Random Song Lyrics :
- maison v(alto maé) - k dirrty 8:30 lyrics
- go - lemmy g lyrics
- kilómetros (primera fila acústico "una última vez - encore") - sin bandera lyrics
- thung thang thung thang churir taale - mrinal chakraborty lyrics
- sug shel ahava - סוג של אהבה - rita - ריטה lyrics
- antologías - ari & el arkeólogo lyrics
- danny myers vs. mike p - urltv lyrics
- denegrir - gabriela oddcast lyrics
- ρούχο λερωμένο (rouho leromeno) - elina konstantopoulou lyrics
- simon sez - clyde mcknight lyrics