
ndidziwe - sagonjah & tadala lyrics
[chorus]
ndidziwe
kodi ndi chikondi
kodi ndi ndalama
kodi ndizadama
funa kukhala limodzi
ndidziwe
ngati ndikufuna, ngati ndikufuna, ngati ndikufuna ndziwe
ngati ndikufuna ndziwe
ngati ndikufuna ndziwe
[verse 1: sagonjah]
kodi tingocheza
ungoyang’ana
malowa ndi a ena
ine mteteza chabe
akuti tingodutsamo
ndisamawelengere
ngati pali msithano
chikondi chikagwere
iwe umandipezelera
umandiseweletsa
umandifuma ndikatentha
chikondi nzichita kupempha
[chorus]
ngati ndikufuna, ngati ndikufuna, ngati ndikufuna ndziwe
ngati ndikufuna ndziwe
ngati ndikufuna ndziwe
ndidziwe
kodi ndi chikondi
kodi ndi ndalama
kodi ndizadama
funa kukhala limodzi
ndidziwe
ngati ndikufuna, ngati ndikufuna, ngati ndikufuna ndziwe
ngati ndikufuna ndziwe
ngati ndikufuna ndziwe
[verse 2: tadala]
ndichani ndisakupanga
ndikuyesetsa kukamba
mwina safila magamba
nde ndumayesa kusamba
kuyesetsa kupanga ngini mmene ukufunira
chamba uzisuta koma uzimeta modulira
ndiwe guy ya bho mwina vuto ndikokulira
ndiwe guy ya bho vuto ndiine uzalira
ndizatonthola ndizayiwala
mpaka ndizatsogola
ndipatse chala
ndati ndikufuna ndidziwe
chif*kwa amene ndikufuna ndi iwe
koma ndisamapoyile chif*kwa ndimafila
mabala amu mtima mwali amatukusira
simayeso nanga bwanji azako amakuuzira
zochita
ati ndine ndika cheater
sungakhale otchipa
nde umandiukira
chikondi chako umachiumira
bwenzi pano theka wandilumira
Random Song Lyrics :
- happy - single version - william bell lyrics
- killing time - droptek lyrics
- testoviron - pet petter lyrics
- homebound - set the score lyrics
- all she's got - mayweather lyrics
- 보석집 (jewelry shop) - qm (korean) lyrics
- duša hrvatska - lana jurčević lyrics
- kingdom - ortiz & dramatone lyrics
- illumination 2014 - linsoluble zairenoi lyrics
- she - isac elliot lyrics