lirikcinta.com
a b c d e f g h i j k l m n o p q r s t u v w x y z 0 1 2 3 4 5 6 7 8 9 #

ona - sagonjah & tadala lyrics

Loading...

[chorus]
nde usalire poti zonse zimatha
usagwedele usakhale ndi mantha
masomphenya, ona masomphenya
mabodza akamaliza zonsezo ndimamva
ndikagwa alipo wina ondiw*nkha
masomphenya, ona masomphenya

[verse 1: tadala]
olenga tulo sangagone
usaganize olenga diso sangaone
usaganize f*kwa umakonda mbewa nde ikasowa olo swiswiri sanganone
i talk to jah my attorney
i’m seeking atonement
sizili yambone
dyomba
dziko kuyenda njomba
kuphana kusaka wapa dziko u karonga
mapiri k*meta mbonga
ili dziko kuwawa
mmitima mwa anthu mw*ngozala chiwawa
achinyamata onyengezedwa mawa
dzikomu kuthawa
tikuchita chani tikapeza power
kuzunza anzathu
kukundikila zotukulira dera lathu
otiyankhulira
ali m’matumba mwa otilamulira
achuluka otigalukila
dziko kulira
mayine toto
tonse tikudziwa
n0body’s immortal
langa ndi loto
tonse tidye mukafaka nkhali pamoto okhulupilira sataya mtima
*n*lenga kuwala *n*lenga mdima
*n*lengayo amandidziwa dzina
ngati lero sizinayendе, zizayende lina
[chorus]
nde usalirе poti zonse zimatha
usagwedele usakhale ndi mantha
masomphenya, ona masomphenya
mabodza akamaliza zonsezo ndimamva
ndikagwa alipo wina ondiw*nkha
masomphenya, ona masomphenya

[verse 2: sagonjah]
chiyembekezo ndimakhulupirira
ngakhale malotowa osagwilika
dikira kuwala kunjaku m’kwam’dima
paning’a pali mdalitso obisika
pambuyo pa mvula utawaleza
gwelo la mphamvu mtima kuwuleza
adani anga amandiyesera
koma opanda mwala sagwedezeka
yang’ana mphoto pambuyo miliri
zilema n*z* mnapulumuka mzambiri
kupita patsogolo mtima ndikulimba
kupasa chete mkuwala utangoima

[chorus]
nde usalire poti zonse zimatha
usagwedele usakhale ndi mantha
masomphenya, ona masomphenya
mabodza akamaliza zonsezo ndimamva
ndikagwa alipo wina ondiw*nkha
masomphenya, ona masomphenya

Random Song Lyrics :

Popular

Loading...