lirikcinta.com
a b c d e f g h i j k l m n o p q r s t u v w x y z 0 1 2 3 4 5 6 7 8 9 #

zima - sagonjah & tadala lyrics

Loading...

[chorus]
ndimakukonda
kukhala ngati kukulondalonda
sinkayika koma ndimawopa
wina azachuluka nzeru uzaf**ka
nkona
zimakhala ngati nsanje
zimakhala ngati nsanje
zimakhala ngati nsanje
zimakhala ngati

[verse 1: tadala]
sindikayika
kuli mtima wako sikutalika
minga yachikondi mayo mtimawu wabayika
nde umaona ngati ndimakusata mapazi
ndikadekha ndekha jenkha manyazi
phone sumandiyankha ndimafoka
ndimafuna pena k*mandikankha
umatalikira
umatayilira
olo namondwe panyanja amakalipira
umandipilira
kupangitsa zinthuzi k*mapitilira
vundula madzi akhoza k*madikira
ndiwe w*nga komabe mtimawu umakusilira
madzi ak*mwa osamapisilira
sanje azikhala nayo mulungu ine ndi nda?
mwina ndikufunika uphungu nde tita?
sanje azikhala nayo mulungu ine ndi nda?
mwina ndikufunika uphungu nde tita?
[chorus]
ndimakukonda
kukhala ngati kukulondalonda
sinkayika koma ndimawopa
wina azachuluka nzeru uzaf**ka
nkona
zimakhala ngati nsanje
zimakhala ngati nsanje
zimakhala ngati nsanje
zimakhala ngati nsanje
zimakhala ngati

[verse 2: sagonjah]
mwina ndi mantha chabe
simmawupeza ndisaname
mwina m’mangawa simnachile ndimilandu yatizibwezi takale
mwina ndi mamuna wansanje
mwina, mwina ndi trauma
chikondi chandiwonetsa zowawa
pano [?] kuteteza mtima w*nga
koma mai mai kalanga
muzitaye zonse ine mmapanga
siine m’ngelo pena ukali
kaduka kuswaya chikondi kutali
koma ngati tingak*mane pakati
tonse tikubwеla kuk*mana mkati
zomwe ndipeleka ndi zomwе ndiyembekeza
[chorus]
ndimakukonda
kukhala ngati kukulondalonda
sinkayika koma ndimawopa
wina azachuluka nzeru uzaf**ka
nkona
zimakhala ngati nsanje
zimakhala ngati nsanje
zimakhala ngati nsanje
zimakhala ngati nsanje
zimakhala ngati nsanje

[bridge]
zimakhala ngati
zimakhala ngati
nsanje
zimakhala ngati
zimakhala ngati
nsanje
zimakhala ngati
zimakhala ngati
nsanje
zimakhala ngati
zimakhala ngati
nsanje
[chorus]
ndimakukonda
kukhala ngati kukulondalonda
sinkayika koma ndimawopa
wina azachuluka nzeru uzaf**ka
nkona
zimakhala ngati nsanje
zimakhala ngati nsanje
zimakhala ngati nsanje
zimakhala ngati nsanje
zimakhala ngati nsanje

Random Song Lyrics :

Popular

Loading...