
black panther party - sevenomore (mw) lyrics
[pre*chorus]
ey*yoh, i’m high (i’m high)
i’m high (i’m high)
somebody say, “i’m high” (i’m high)
[chorus]
it’s a black panther party
black panther party
it’s a black panther party
black panther party
it’s a black panther party
black panther party
it’s a black panther party
black panther party
[verse 1]
down on my knees
k*mpempha mlungu
ambuye chonde ngwileni nkono
nkhondo ndayiyambayi
pandekha sindingathe
kuli angelo, anzake a satana
akundinong’oneza, akundisokoneza
andionetsa dziko
ati landikulira
ati nchif*kwa chake ine ndiwobalalika
ati nchif*kwa chake zinthu zimatikanika
koma nkati tachoka, tachoka, tachoka
kamabwera kenanso, tachoka
kubwera ka ulesi, tachoka
kubweranso ka mantha, tachoka
oh my god
[?]
dj ta mixer ya gina ilipati?
[pre*chorus]
ey*yoh
i’m high
i’m high
i’m high
[chorus]
it’s a black panther party
party, party
it’s a black panther party
party, party
it’s a black panther party
party, party
it’s a black panther party
party, party
[verse 2]
nakafikako, nakawonako
tingoti ndinakachezako
ku babiloniko nakagonako
tingoti tinakawonako
malamulo aja anangowasintha
[?]
there’s a land far, far away
it’s called addis ababa
Random Song Lyrics :
- war in me - electro king lyrics
- muscle beach - surf dads lyrics
- take time to know me - spencer lyst lyrics
- til mine øjne bløder - mikkel mund lyrics
- slo rock - gundelach lyrics
- moonstruck - sean handley lyrics
- cobras - kafv lyrics
- abbot kinney - jake bosci lyrics
- mr ar0chet - mortal lyrics
- untold story - shakes lo lyrics