
akanadziwa - suckle lyrics
intro(hezel kanyamwale)
na na na na na!! akanadziwa!!(malume!)
suckle!! kanyamata kanyamwale…
its your boy hezel!
verse 1(suckle)
akanadziwa//
kulira pa mtanda paja -n-li machimo athu olemetsa//
akanadziwa//
kudzuka tsiku lachitatu unali ulemerero oti wagonjetsa imfa//
aaa iwe!!ukamba za yesu bwanj asanakufere iwe!!//
ati son of the most high ukamba za munthu iwe! //
ka blessing ka yesu mwasanduka nako yesu nanu//
mukanadziwa bruh u couldn’t even bother//
mukan-z-ndikira sibwezi muli aboza//
yesu amatikonda kukonda koposa kukonda//
sunabwera pa dziko kudzanjoya chinyamata//
u we’re born with a purpose kuombora a mantha
hook(hezel kanyamwale)
akanadziwa!!,,,,//
anzawo akupemphera iwo akuyesa za nthabwala,,,,
awa!!! hayeeeee,,,//
akanadziwa!!!!,,,,
kuti yesu ndiye mpulumutsi,, anafa kamba ka ife,,,,
akanangosiya tchimo!! //
verse 2(suckle)
aaa! koma anakati kukhala amatere//
ndithu amwene sanakatichotsa mndende//
kudzichepetsa kuti ndiwafere//
mpamene machimo akuterera ngati aponda ndele//
tele dele akanadziwa sakanayesera olo pang’ono kuti kuti amumvere//
mdyerekezi akuwaphuza mkhalidwe oti aledzere//
mukanadziwa amamva kuwawa mumtima//
chif-kwa chachikondi nkona samagiva//
amatipemphera iye samayimva//
ndizachisoni aunt muchedwa ndi u diva//
mukanadziwa sibwezi muli choncho mukanapanga chiganizo sister//
nde mutsalatu eya tikupita//
hook(hezel kanyamwale)
akanadziwa!!,,,,//
anzawo akupemphera iwo akuyesa za nthabwala,,,,
awa!!! hayeeeee,,,//
akanadziwa!!!!,,,,
kuti yesu ndiye mpulumutsi,, anafa kamba ka ife,,,,
akanangosiya tchimo!! //
Random Song Lyrics :
- money - p.black mr. international lyrics
- happy halloween (prod. by lil flighty) - lil dae dae lyrics
- dale - fernandocosta lyrics
- polak rusek i niemiec - lao che lyrics
- ハシタイロ (hashita-iro) - rionos lyrics
- chartreuse - collapsis lyrics
- grey - emilie brandt lyrics
- horizons - the uncharted (uk) lyrics
- a message from dj paul (skit) - yelawolf lyrics
- pompeii (arcando & afterfab remix) - bastille lyrics