
intro - suckle lyrics
Loading...
ine ndimagona//
kudzuka osalota//
osamanditchula star sindimafuna kuwala chikoka//
ndimayenda ndicholinga pano ndi abraz//
thupili ndi temple mokhala okhetsa mwazi//
mtendere ndikusangalala zokhaso basi//
ayi njee kugawa mawu ndicholinga chathu//
eeh eya ma guy ndinewakhama ngini zanga zimayenda mwa kaya//
sorry ma guy ndilibe chuma koma za dziko nde zimandig*ya//
zimandinyenya zimandiphwanya//
mtima odzadza ndi dama chandichosera ch*nkhwaya//
awo kaya yesu w*nga wauka//
*n*li ndi mwayi oborna ona pano awutaya kupembedza chauta//
chomwe nnakhazikitsa mu mtima mw*nga inu kaya//
checka boldness ase koma suckle ndiwakhama//
ladies and gentlemen!
welcome to sleep without dreams extended playlist!
Random Song Lyrics :
- lyrics are hard - nuggos lyrics
- sky green - jiwoo (지우) lyrics
- 별비그대 *:・゚ (rain star *:・゚) - yongyong (용용) lyrics
- motive - santoro keyz lyrics
- to moje życie - krzysztof krawczyk lyrics
- imperfect. - figoshin lyrics
- led myself on - liddy clark lyrics
- waiting for a stranger - geographer lyrics
- easiest ballroom dance - jesadn lyrics
- lettre - bulk requiem lyrics