
tilimomo challenge - suckle lyrics
verse
sitinavenche ndife amomo olo panja sipatidziwa(heee!!)//
moyo wosatha ndi wakuuzimu olo kuthupi nditadiwa(heee!!)//
unandiyelesa paja ndi mwazi sitinasambe madziwa(haaa!!)//
pano ndinagontha nkhuthu sinding-yimbe zanuzo zonzimva//
hehe!ndili momo adha mmene ndalowera mwachisomo adha//
ndimawu okha nyanja bata ati sitichita mantha nanga achani adha//
tilimomoka (eyah!!)//
ena pompa akukomoka (pepani!!)//
ati bola timafirika ndechan(ndechani?))//
you be the most high,you call yourself fly//
ati ndiofewa kuposa sofayi//
kuyiwala yemwe anawafera//
momo watsegula kh-m- zikomo manong’onong’o//
apang’ono madolo osavera kholo pakh-m-//
lamwamba sakagunda olo tsogolo lanulo//
lopanda lamulo iwaya ya dzulo taona za uyo owona za lero//
Random Song Lyrics :
- depresión - batu (metal band) lyrics
- biba - żabson & kronkel dom lyrics
- 9 mm uzi - isk lyrics
- all inclusive - msk real og lyrics
- i paid a hooker in robux - 2worth lyrics
- беззубие (toothless) - lida & mzlff lyrics
- zero - laura pausini lyrics
- changed who i was - ctb dru lyrics
- never say never - kodyiskool lyrics
- i miss u - henry moodie lyrics