lirikcinta.com
a b c d e f g h i j k l m n o p q r s t u v w x y z 0 1 2 3 4 5 6 7 8 9 #

kwanu nkwanu - suffix (mwi) lyrics

Loading...

[intro:]
listen

[verse 1:]
bambo anga ankandikhazika
pansi, ndili mwana wovuta
ndili chakusekondale heee ndisakuganizaso zoyimba
mwana w*nga ndithu kukula
ife taonapo yambili mvula
ndiwe first born ife tikudalila, ukafuntha uzapita mwachangu k*manda
kusukulu komwe uliko, uzik*mbuka komwe uchokela
nanenso nnali ndiazizanga ambili sindziwa komwe *n*lowela

[chorus:]
dziwa dziwa dziwa, mwana w*nga
dziwa dziwa dziwa, mwana w*nga
dziwa dziwa mwana w*nga
dziwa dziwa, mwana w*nga
kwanu nkwanu nkwanu
mwana w*nga, kwanu nkwanu nkwanu
mwana w*nga, kwanu nkwanu
mwana w*nga, kwanu nkwanu nkwanu
mwana w*nga
heeehhh

[post*chorus:]
hee huhu
hee huhu
hee huhu
hee huhu
[verse 2:]
yea, life sikhala fair
macritisism sabweletsa sheda
aliyense ali nzokonda zake, akadana ndizokonda zako usamawatengela
k*masiyanitsa azako ndiabale
ena utavutika sangathandize m’bale
osamatengeka akamakuchemelera
enawo ukazazizila azakupanga chandamaleee

[chorus:]
dziwa dziwa dziwa, mwana w*nga
dziwa dziwa dziwa, mwana w*nga
dziwa dziwa mwana w*nga
dziwa dziwa, mwana w*nga
kwanu nkwanu nkwanu
mwana w*nga, kwanu nkwanu nkwanu
mwana w*nga, kwanu nkwanu
mwana w*nga, kwanu nkwanu nkwanu
mwana w*nga
heeehhh

[post*chorus:]
hee huhu
hee huhu
hee huhu
hee huhu
[outro:]
dziwa dziwa dziwa, mwana w*nga
dziwa dziwa dziwa, mwana w*nga
dziwa dziwa mwana w*nga
dziwa dziwa, mwana w*nga
kwanu nkwanu nkwanu
mwana w*nga, kwanu nkwanu nkwanu
mwana w*nga, kwanu nkwanu
mwana w*nga, kwanu nkwanu nkwanu
mwana w*nga
heeehhh

Random Song Lyrics :

Popular

Loading...