lirikcinta.com
a b c d e f g h i j k l m n o p q r s t u v w x y z 0 1 2 3 4 5 6 7 8 9 #

mama - trappy beats lyrics

Loading...

[intro]
ndikudziwa ndinachoka kale
munandiona kale
(eya kale kale)

[verse 1: trappybeats.]
ndinachoka kupita kutali
kukasaka mwayi
(amayi amayi)
ndikak*mbuka munkanena
zizandiyendera
nkusintha moyo wanu mama
ndinali mwana sind*nkamvesa
zoipa munkandilesa
nkundilimbikisa mama

[refrain: trappybeats.]
oh, oh, oh
oh, oh, oh
oh, oh, oh

[verse 2: hope cizzle.]
ndinakulonjezani masion
mus*n*landile pension
ku suncity
inu ndi bigman vacation
koma osaona kuchedwa
ndikuphusha zikutheka
sooner or later
you will be eating my paper
it’s okay kaya ndigudumuka mumatope
busy working all day
cause i know my work is gonna pay off
it’s okay kaya ndigudumuka mumatope
busy working all day
cause i know my work is gonna pay off
[refrain: trappybeats.]
oh, oh, oh
oh, oh, oh
oh, oh, oh

Random Song Lyrics :

Popular

Loading...