lirikcinta.com
a b c d e f g h i j k l m n o p q r s t u v w x y z 0 1 2 3 4 5 6 7 8 9 #

manyazi - twnda lyrics

Loading...

[intro:]
ta*ta ta*la*ta ta*la*ta ta
ta*ta ta*la*ta ta*la*ta ta
eh

[verse 1:]
i won’t say much, l just cut to the chase
i broke your heart and l just fell away
we were not lovers, no, we were real friends
i hate the way that i put this to bed

[chorus:]
ndimakuona mu ma instagram, yeah
uli ku nyanja utabhebha
zako zonse zikuyenda
ndimakuona mu ma whatsapp, ma status
kulakalaka nditacommenta, ndithudi mamie
nditacommenta

koma ndekha manyazi (manyazi, manyazi)
koma ndekha manyazi (manyazi, manyazi)
inu ndekha manyazi (manyazi, manyazi)
inu ndekha manyazi (manyazi, manyazi, koma ndekha manyazi)

[verse 2:]
ife anthu timapanga ma plan (ma plan)
mulungu naye amangoseka (ha ha ha)
nkadadziwa kalero, nkadapewa za lero
[chorus:]
ndimakuwona mu ma instagram (ndimakuwona)
uli ku nyanja utabhebha
zako zonse zikuyenda
ndimakuona mu ma whatsapp, ma status
kulakalaka nditacommenta, ndithudi mamie
nditacommenta

koma ndekha manyazi (manyazi, manyazi
ndimakuwona)
koma ndеkha manyazi (manyazi, manyazi)
inu ndekha manyazi (manyazi, manyazi)
inu ndekha manyazi (manyazi, manyazi, koma ndekha manyazi)

[outro:]
koma zimanyazi zimandigwira
ohh, ndikak*mbukira

Random Song Lyrics :

Popular

Loading...