
chopambana - vicente jr. lyrics
*natamanda nikulupilila napeza chikondi chake chopambana
*sinikana nikulupilila napeza chikondi chopambana
* napeza chikondi chopambana
*chikondi chopambana
mutinta wenzo nkala usakila lyonse
kuyesa nenzo yesa
lomba nibsni banikonde
koma chikondi cha zoona
sichinama sichongazima sichisila
lokokutulo kweka
nizakutokozani bwanji
pachikondi mwanipasa
nizakutamandani bwanji
pali okondewa w*nga
nikulupilila napeza chikondi chake
chopambana
* napeza chikondi chopambana
*chopambana
*chikondi chopambana
*chopambana
*chikondi chopambana
*natamanda nikulupilila napeza chikondi chake chopambana
*sinikana nikulupilila napeza chikondi chopambana
* napeza chikondi chopambana
*chikondi chopambana
a fish out of water that is me without you fighting for my life to prove my love is true call me boo*boo and i will call you bae this love is so sweet and i am here to stay your smile guarantees a nice and happy life weh chintelelwe chandi
i want to hold you tight kiss you through the night now that you are my wife i will love you now and forevеr and never out of sight virtuous a beauty at thе sight of man i am responsible i’m feeling like i’m supermanbut what is me without christ and you by my side so i secure this union the holy ghost ndetasha lesa nampala double double aba kashi nabana elo nshakane ine ninkeana thank god for this blessing lelo ndeshana
*chopambana
*chikondi chopambana
*chopambana
*chikondi chopambana
*natamanda nikulupilila napeza chikondi chake chopambana
*sinikana nikulupilila napeza chikondi chopambana
* napeza chikondi chopambana
*chikondi chopambana
Random Song Lyrics :
- gorgeous pt. 1 - b.l.b.p. lyrics
- that's how mafia works - lil citrus p lyrics
- c'est pas grave papa - jean-jacques goldman lyrics
- retour en solo - biale roze lyrics
- mala cabeza - maria toledo lyrics
- t2 - timbuktu lyrics
- on my mind - disciples lyrics
- this is hip hop - lecxs ahziz lyrics
- shadows - los gold fires lyrics
- hank moody - kuban lyrics