lirik lagu chinsapple -freestyle – crispy malawi
[intro]
cheo meek
uhhhhh ooohh
chinsapo
mad beats
[chorus]
ndamva you looking for me
mubwere ndi ma friends mundipeza ku chinsapo
airforce ili clean ndavala white tee koma ndiku choka kwa chinsapo
ku chinsapo
ndili ghetto ngati mchesi ndi chinsapo
nde ukazapwekesanso chinsapo izakupanga chitsanzo
[verse]
i pray to god my soul to keep
kwa sumanje kwa dzombe kukagula weed[?]
amandifila amandiwona pa screen
or ndikayika drip ngat mfana wa teams[?]
koma ndachoka kwa chinsapo
komwe ma babie amagomera bado
ngati samayaka amangofuna bundle
gang yanga ma dentist izakuchotsa mano
[bridge]
chinsapo
chinsapo
chinsapo
chinsapo
chinsapo
chinsapo
[chorus]
ndamva you looking for me
mubwere ndi ma friends mundipeza ku chinsapo
airforce ili clean ndavala white tee koma ndiku choka kwa chinsapo
ku chinsapo
ndili ghetto ngati mchesi ndi chinsapo
nde ukazapwekesanso chinsapo izakupanga chitsanzo
[verse 2]
ndingotula ndima gees[?]
bola trizer i got the keys[?]
ndipo ukuziwa kale ndimakhala busy
undihalla chama three mwina nditha kukhala free
komabe ase ukuziwa sitinga chille
i gotta tell your straight ndisakubisile
i’m moving smart koma sindimapisila
and i’m talking sh*t koma sindin*z*pisire
ndimamenyaso ma punch guys wina andigwire
gist imandikhala ngati mpando
you can’t walk in my shoes uzingovala sandals
money talks mphw*nga usachulutse nthano
mukatinter ngati spe musachulutse kano
[chrous]
ndamva you looking for me
mubwere ndi ma friends mundipeza ku chinsapo
airforce ili clean ndavala white tee koma ndiku choka kwa chinsapo
ku chinsapo
ndili ghetto ngati mchesi ndi chinsapo
nde ukazapwekesanso chinsapo izakupanga chitsanzo
cheo meek you’ve been k!lling it hihihihi
lirik lagu lainnya :
- kumpulan lirik lagu micko swag › lirik lagu hard trap – micko swag
- kumpulan lirik lagu smb › lirik lagu little bitch – smb
- kumpulan lirik lagu mylittlethumbie › lirik lagu lilies – mylittlethumbie
- kumpulan lirik lagu a lin twn › lirik lagu 抱歉,我不抱歉 (i’m not sorry) – a-lin (twn)
- kumpulan lirik lagu john west nl › lirik lagu alles wat ik wil – john west (nl)
- kumpulan lirik lagu troy kingi › lirik lagu predetermined machine – troy kingi
- kumpulan lirik lagu author › lirik lagu music – author
- kumpulan lirik lagu freshfact › lirik lagu сон 2020/аутро (dream 2020/autro) – freshfact
- kumpulan lirik lagu tarek zenci › lirik lagu flavours 3: risky – tarek & zenci
- kumpulan lirik lagu wjsn the black › lirik lagu kiss your lips – wjsn the black