lirikcinta.com
a b c d e f g h i j k l m n o p q r s t u v w x y z 0 1 2 3 4 5 6 7 8 9 #

lirik lagu international spe -freestyle – crispy malawi

Loading...

[verse]
nnangodzuka mornaz ndi zi confi za ine
nnamu talker jah jah ndizijama ya ine
anangoti udekhe ndikupanga za iwe
11:11 i got blessings on the way
goat wanu ati aku payer ma page
kuti apange damage za dancehall ya ine
ndinali ku naisi ndi boys ya ine
nditaona nnangoseka ndikuzitaya ine
rolex ili pa bwanji ino ndi nthawi ya ine
born ready ondichedwesa ndim*th*wa ine
good vibes usandipatse nkhawa ine
international spe iwe si makawa ine
mtv base ku player step by step
back to back
sindimvela nyimbo zanu, chif*kwa chani?
ndi za whack
cash ima talker yokha choka phw*nga ulibe cash
busy pocket watching koma dollar sili mu thumba
ndikupanga zanga inu mungosilira
mulimbe mtima guys mungopilira
ndilipo mpaka nzachita kusankha omusiyila
dollar ya show ingokwela ngati katapila
best mc in mdubz
kuyambitsa chipwilikiti pa entrancе
8o8 wa beat kusokoneza neighbour
trap bidnеss ku trap osabwela ndi chikheba
i’m too good at this
iwe uk*mvela ziti?
utalker ziti?
zaza pa repeat uku uku burner ah
cannabis
your goat can’t trap like this
zosafila spe ndizachimidzi

lirik lagu lainnya :

YANG LAGI NGE-TRENDS...

Loading...