lirikcinta.com
a b c d e f g h i j k l m n o p q r s t u v w x y z 0 1 2 3 4 5 6 7 8 9 #

lirik lagu tsidya lina – mistah yemie

Loading...

[intro]
mmmm yeah, yeaii(yeaii)
osaleka kusaka
inu ndine tisagive nsanga
tings will be tswayi
oyoo yii

[hook]
tizak*mana tsiku lina
ku tsidya lina
ndipo tizak*mbutsana
momwe tinka vutikira

pok*mbutsana nk*maseka, tears of joy
“tears of joy”
tears of joy ooii, tears of joy
“tears of joy”

[verse 1]
yeaii
tiziza k*mbutsana momwe tinkavutikira
back when we got nothing, tilibetu pogwira
tizizango fila kupasana ka chears
tik*mwa champaine, tikuk*mbuka kachasu

on that side life is gonna be great
everyting okay
atayankha ma prayer
k*mango k*mbukira kenako nk*mangoseka
hard work italipira titayalura mikeka
[hook]
tizak*mana tsiku lina
ku tsidya lina
ndipo tizak*mbutsana
momwe tinka vutikira

pok*mbutsana nk*maseka, tears of joy
“tears of joy”
tears of joy ooii, tears of joy
“tears of joy”

[verse 2]
yeaii
moyo uzakoma
titagonjetsa zokhoma
tiza leader life ngati tinalowa m’boma
man a ghetto yut oti alibe deproma
osa user mfuti koma kuyendera beamer

kuwolokeratu man
k*mango spender money
new bens deh deh
ndizi mandede
get a big mansion fi mi parents deh deh
one billion dollar in a mi acount deh deh
[hook]
tizak*mana tsiku lina
ku tsidya lina
ndipo tizak*mbutsana
momwe tinka vutikira

pok*mbutsana nk*maseka, tears of joy
“tears of joy”
tears of joy ooii, tears of joy
“tears of joy”

[bridge]
yeaii
osaleka kusaka
inu ndine tisagive nsanga
tings will be tswayi
oyoo yii

on that side life is gonna be great
everyting okay
atayankha ma prayer
k*mango k*mbukira kenako nk*mangoseka
hard work italipira titayalura mikeka

[hook]
tizak*mana tsiku lina
ku tsidya lina
ndipo tizak*mbutsana
momwe tinka vutikira
pok*mbutsana nk*maseka, tears of joy
“tears of joy”
tears of joy ooii, tears of joy
“tears of joy”

lirik lagu lainnya :

YANG LAGI NGE-TRENDS...

Loading...