lirik lagu lalala – namadingo
[intro: namadingo]
alipo, alipo ondi*
alipo, alipo ondi*
[verse 1: namadingo]
alipo ondidelera
m’maso mwawo ndimachepera
akuti nyimbo zanga samvera
ndi*ndi, ndipo sine oyenera k*manditchula dokotala
ndilibe phd papepala
angondipatsa udokotalawu
nde wina akamva doc sasangalala
eti mpaka kunditchula kuti wamsala
ndingothokoza mulungu oyera amandikondera
madalitso akubwera tikulemera
namadingo most followed mumfuse [?]
[chorus: namadingo]
adzavomeleza too late (pano iwo ndi lalala)
kuti mwana uja ndi dolo (pano iwo ndi lalala)
koma too late, too late, too late (pano iwo ndi lalala)
koma too late, too late, too late (pano iwo ndi lalala)
[verse 2: ty grin & namadingo]
rrr*rah, dats de fire dere
mfumu yazinyawu ija
flow so sick i need a doctor to feature
i am not an average joe, they pay me what you make in a year for a show
in a deck of cards i’m the jokеr
i’m the extremе opposite of mediocre
simungamake ndine messi pa soccer
grin ndi messi pa soccer (yeah)
too many international awards
i’m representing malawi, your bro
doing this till i grow old
nanga time squires? ndili pa billboard
[chorus: namadingo]
ena adzavomeleza too late (pano iwo ndi lalala)
kuti mwana uja ndi dolo (pano iwo ndi lalala)
koma too late, too late, too late (pano iwo ndi lalala)
koma too late, too late, too late (pano iwo ndi lalala)
ena adzavomeleza too late (pano iwo ndi lalala)
kuti mwana uja ndi dolo (pano iwo ndi lalala)
koma too late, too late, too late (pano iwo ndi lalala)
koma too late, too late, too late (pano iwo ndi lalala)
[verse 2: ty grin & namadingo]
muliponso ena all over the world
mumadeleledwa kuchepetsedwa
if you visualize it, you’re bound to do it
life’s a jungle, me i rumble through it
if i can do it, y’all can do it
from the frontline, put your back into it
[chorus: namadingo]
ena adzavomeleza too late (pano iwo ndi lalala)
kuti mwana uja ndi dolo (pano iwo ndi lalala)
koma too late, too late, too late (pano iwo ndi lalala)
koma too late, too late, too late (pano iwo ndi lalala)
ena adzavomeleza too late (pano iwo ndi lalala)
kuti mwana uja ndi dolo (pano iwo ndi lalala)
koma too late, too late, too late (pano iwo ndi lalala)
koma too late, too late, too late (pano iwo ndi lalala)
[outro: ty grin]
joe gwaladi aseh uli bho?
lirik lagu lainnya :
- kumpulan lirik lagu new interstates › lirik lagu last night – new interstates
- kumpulan lirik lagu suede tyrell › lirik lagu cold steppa – suede tyrell
- kumpulan lirik lagu giraffage › lirik lagu maybes (edit) – giraffage
- kumpulan lirik lagu миа бойка mia boyka › lirik lagu мизинчик (little finger) – миа бойка (mia boyka)
- kumpulan lirik lagu tigaro and monsey › lirik lagu ily – tigaro and monsey
- kumpulan lirik lagu noxthyn › lirik lagu twentynineteen – noxthyn
- kumpulan lirik lagu officialblankstate › lirik lagu pale blue – officialblankstate.
- kumpulan lirik lagu omniq › lirik lagu no more – omniq
- kumpulan lirik lagu ace og › lirik lagu we gon win – ace og
- kumpulan lirik lagu jo bmb h › lirik lagu cinematic – jo (bmb-h)