lirikcinta.com
a b c d e f g h i j k l m n o p q r s t u v w x y z 0 1 2 3 4 5 6 7 8 9 #

lirik lagu kuthokoza – sagonjah & tadala

Loading...

[intro :sagonjah]
kunja kwacha, dzuwa latuluka. anthu alowe komwe amasaka ndalama, eeh, koma tisananyamuke k*mathokoza mulungu mu zonse eeeh

[verse 1 :tadala]
kuyamika mu zonse ngakhale zonse ndi chabe
zisachite kufika poti mpakana ndikabe
zochepazi ziph*kile
mtima w*nga ukhutile
ngati chinga gile nkabwelela mundichingamile
zinsinsi za moyo mundiululire
zipatso za moyo mundipululire
moto wanyanya nkhuni mutifumilile
dziko kuzungulira osadabwa zizungulire
sink*mila ndikuyandama
osaodzela ndikuyang’ana
zisomo zake zingotsagana
ndinali yani dzana
lero ndine nyali dzana timangonamizana
sinditama munthu kuwopa mwina andimana
mu m’bwaa zanga ukhwepa
panga zaine mpakana mtembo useka
k*mbwambwana ambwana
k*mazinyenga kupambana
zako nzake zake namana k*mkhwapa napana

[hook: sagonjah]
lero ndingothokoza
(yes faddah)
mu zonse inu nditsogoza
kusekelera otonza
sazagwesedwa odzodza
[verse 2: sagonjah]
chida changa ,chili ma wondo
ndizake izi amamenya yekha nkhondo
kuno ndi uko ntambasale
ndiziwopa chani poti alinane
alinafe …akapanga zaifeyo alinaye
sanayambe walepherapo ake
isandlwana kapena adwa
kwayiyeyo olo jabulo amagwada
watipasa moyo ,chigwa chanthuzi wa infa
chitetezo cha duwa pakati pa minga
monga langa linga ,zambiri zopinga koma ndinu nokha mungamasulile zanga nsinga
ndi zopanda ntendere njira za dziko
diso kwa diso ,dzino kwa dzino
mangawa ndi chimo ,chanu chik*mbuntima
sizafike poteteza saya lina

[hook: sagonjah]
lero ndingothokoza
(yes faddah)
mu zonse inu nditsogoza
kusekelera otonza
sazagwesedwa odzodza
zonse ndizayasa pososa

lirik lagu lainnya :

YANG LAGI NGE-TRENDS...

Loading...