lirikcinta.com
a b c d e f g h i j k l m n o p q r s t u v w x y z 0 1 2 3 4 5 6 7 8 9 #

lirik lagu tafika – trim sky

Loading...

tafika tafika
tafika tafika
spinsol on the beat

oni konda monga amama
i can′t believe ndiwe nilangana
oni sunga monga mwana
una nikonda nilibe ndalama
tiyende pamodzi niku peleke kwa amama
osalema tili k*ma peto
chikindi pa scale ni finger na ka ring
yeah! hah!
my heartbeat mood changer
rain or shine tilice pamozi
for better for worse
why should i keep on waiting
long time dating
let me now make a purchase
peace maker
ever since you came in my life
you give me peace of mind
you took all my insecurities
tafika
apa ni pamepene tafika tafika
tafika
apa nipanopene tafika tafika
maphiri takwela misinje ku mbuyo
apa manje tafika
maphiri takwela misinje ku mbuyo
apa manje
tafika tafika
tiye ku sogo osalanga ku mbuy
tafika tafika
maphiri takwela misinje ku mbuyo
tafika tafika
tiye ku sogo osalanga ku mbuy
tafika tafika
maphiri takwela misinje ku mbuyo
apa manje
tafika
mayeso navina tagwesa
singa bise mpepe ikacaya wenzeko
nanvula inga bwele sindi wala
tafika nafika
amai landilani tafikak
kanchito kuliko kabandi namange
apa manje naleta
amai landilani
monga nikulota
mabanja pamozi acheza
ona ce kuseka
monga kwenze libe ma issue
seka manso uni ona
am on the alter waiting for you
seka manso uni ona
am on the alter waiting for you
what a beautiful day
girl you’re looking beautiful in white
coming from afar
never been easy
to stay in love with you
but you make it easy for to love you
i aren′t scared of anything
cause i gat you in my life
tafika
apa ni pamepene tafika tafika
tafika
apa nipanopene tafika tafika
maphiri takwela misinje ku mbuyo
apa manje tafika
maphiri takwela misinje ku mbuyo
apa manje
tafika tafika
tiye ku sogo osalanga ku mbuyo
tafika tafika
maphiri takwela misinje ku mbuyo
tafika tafika
tiye ku sogo osalanga ku mbuy
tafika tafika
maphiri takwela misinje ku mbuyo
apa manje

lirik lagu lainnya :

YANG LAGI NGE-TRENDS...

Loading...